Lirik Lagu Mwazi The Very Best

Gabung member, untuk simpan koleksi lirik lagu favorit anda Disini

Ukakhala Iwe Mphwanga
Usadzinamize Uli Ndi Abale
Amakukonda Uli Ndi Chuma
Ukasauka Kukutaya
Amayiwala Kuti Mwazi Ndi Mwazi
Umawundana Kuposa Madzi

Iwe Iwe Mvera
Tchera Tchera Khutu
Ganiza Ngati Munthu
 

 
  The Very Best   Reposted by Admin  79x     2024-12-23 12:29:04

post a comment